Mlaliki 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimene zilipo zinalipo kale, ndipo zimene zidzachitike zinachitikapo kale.+ Mulungu woona+ amafunafuna kuchitira zabwino anthu amene akuzunzidwa.+
15 Zimene zilipo zinalipo kale, ndipo zimene zidzachitike zinachitikapo kale.+ Mulungu woona+ amafunafuna kuchitira zabwino anthu amene akuzunzidwa.+