1 Mafumu 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nzeru za Solomo zinaposa+ nzeru za anthu onse a Kum’mawa+ ndi nzeru zonse za ku Iguputo.+ Miyambo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ukamvetsera nzeru ndi khutu lako,+ ukaika mtima wako pa kuzindikira,+ Mlaliki 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+ Mlaliki 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mogwirizana ndi zimenezi ndinatsimikiza mumtima mwanga+ kuti ndidziwe nzeru ndiponso ndione ntchito imene ikuchitika padziko lapansi,+ chifukwa alipo amene sagona tulo usana ndi usiku.+
25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+
16 Mogwirizana ndi zimenezi ndinatsimikiza mumtima mwanga+ kuti ndidziwe nzeru ndiponso ndione ntchito imene ikuchitika padziko lapansi,+ chifukwa alipo amene sagona tulo usana ndi usiku.+