Yobu 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Aang’ono ndi aakulu amakhala chimodzimodzi kumeneko,+Ndipo kapolo amamasuka kwa mbuye wake. Yobu 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mwamuna wamphamvu amafa ndipo amagona pansi atagonjetsedwa.Munthu wochokera kufumbi amatha. Kodi ali kuti?+ Mlaliki 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mapeto ngati a munthu wopusa+ adzagweranso ineyo ndithu.”+ Choncho kodi ineyo ndinavutikiranji kukhala wanzeru kwambiri+ pa nthawi imene ija? Ndipo ndinanena mumtima mwanga kuti: “Izinso n’zachabechabe.”
10 Koma mwamuna wamphamvu amafa ndipo amagona pansi atagonjetsedwa.Munthu wochokera kufumbi amatha. Kodi ali kuti?+
15 Ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mapeto ngati a munthu wopusa+ adzagweranso ineyo ndithu.”+ Choncho kodi ineyo ndinavutikiranji kukhala wanzeru kwambiri+ pa nthawi imene ija? Ndipo ndinanena mumtima mwanga kuti: “Izinso n’zachabechabe.”