Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Genesis 47:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndikufuna ndikagone limodzi ndi makolo anga.+ Choncho udzandinyamule ku Iguputo kuno, ukandiike m’manda a makolo anga.”+ Yosefe anayankha kuti: “Ndidzachitadi monga mwa mawu anu.” Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
30 Ndikufuna ndikagone limodzi ndi makolo anga.+ Choncho udzandinyamule ku Iguputo kuno, ukandiike m’manda a makolo anga.”+ Yosefe anayankha kuti: “Ndidzachitadi monga mwa mawu anu.”
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .