Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ 1 Akorinto 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Popeza imfa+ inafika kudzera mwa munthu mmodzi, kuuka+ kwa akufa kunafikanso kudzera mwa munthu mmodzi.
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
21 Popeza imfa+ inafika kudzera mwa munthu mmodzi, kuuka+ kwa akufa kunafikanso kudzera mwa munthu mmodzi.