Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 88:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi anthu akufa mudzawachitira zodabwitsa?+

      Kapena kodi anthu akufa, anthu amene sangachite kanthu, adzauka?+

      Kodi adzakutamandani?+ [Seʹlah.]

  • Salimo 115:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Akufa satamanda Ya,+

      Ngakhalenso aliyense wotsikira kuli chete.+

  • Salimo 146:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+

      Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+

  • Yesaya 38:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+

      Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+

  • Yohane 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena