Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Sadzabwereranso kunyumba yake,

      Ndipo anthu a pamalo ake sadzamuzindikiranso.+

  • Salimo 109:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+

      Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+

  • Mlaliki 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti munthu wanzeru, mofanana ndi wopusa, sadzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ M’masiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalidwa. Ndipo kodi wanzeru adzafa motani? Adzafa mofanana ndi wopusa.+

  • Yesaya 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena