Miyambo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kuzizira, waulesi salima.+ Iye azidzapemphapempha nthawi yokolola koma sadzapatsidwa kanthu.+ Miyambo 24:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 umphawi wako ndithu udzabwera ngati wachifwamba ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+
4 Chifukwa cha kuzizira, waulesi salima.+ Iye azidzapemphapempha nthawi yokolola koma sadzapatsidwa kanthu.+
34 umphawi wako ndithu udzabwera ngati wachifwamba ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+