Yobu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munandiveka khungu ndiponso mnofu,Ndipo munandiluka ndi mafupa ndi mitsempha.+ Salimo 139:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu munapanga impso zanga,+Ndipo munali kunditchinga m’mimba mwa mayi anga.+ Salimo 139:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi. Yeremiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”
15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi.
5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”