Yobu 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkazi wanga aperere ufa mwamuna wina,Ndipo amuna ena agone naye.+ Yesaya 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tenga mphero+ upere ufa. Vula nsalu yako yophimba kumutu.+ Vula chovala chako chokhwekhwerera pansi.+ Ukweze chovala chako m’mwamba mpaka miyendo ionekere,+ ndipo uwoloke mitsinje. Mateyu 24:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Akazi awiri adzakhala akupera pamphero+ wina adzatengedwa ndipo winayo adzasiyidwa.+
2 Tenga mphero+ upere ufa. Vula nsalu yako yophimba kumutu.+ Vula chovala chako chokhwekhwerera pansi.+ Ukweze chovala chako m’mwamba mpaka miyendo ionekere,+ ndipo uwoloke mitsinje.