Salimo 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Adzamubweretsa kwa mfumu atavala chovala choluka.+Anamwali anzake omuperekeza akubwera nawo kwa iwe.+ Chivumbulutso 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+
14 Adzamubweretsa kwa mfumu atavala chovala choluka.+Anamwali anzake omuperekeza akubwera nawo kwa iwe.+
7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+