Mateyu 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atanyamuka kupita kukagula, mkwati anafika, ndipo anamwali okonzekerawo analowa naye limodzi m’nyumba imene munali phwando laukwati,+ ndipo chitseko chinatsekedwa. Chivumbulutso 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+
10 Atanyamuka kupita kukagula, mkwati anafika, ndipo anamwali okonzekerawo analowa naye limodzi m’nyumba imene munali phwando laukwati,+ ndipo chitseko chinatsekedwa.
9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+