Nyimbo ya Solomo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Masaya ake ali ngati bedi la m’munda la maluwa onunkhira,+ ndiponso ngati nsanja zomangidwa ndi zitsamba zonunkhira. Milomo yake ili ngati maluwa amene akuchucha mafuta a mule.+
13 Masaya ake ali ngati bedi la m’munda la maluwa onunkhira,+ ndiponso ngati nsanja zomangidwa ndi zitsamba zonunkhira. Milomo yake ili ngati maluwa amene akuchucha mafuta a mule.+