Salimo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Psompsonani mwanayo+ kuopera kuti Mulungu angakwiye,Ndipo mungawonongeke ndi kuchotsedwa panjirayo.+Pakuti mkwiyo wake umatha kuyaka mofulumira.+Odala ndi onse amene akuthawira kwa iye.+ Nyimbo ya Solomo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Undipsompsone ndi milomo yako,+ chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo kukoma kwake.+
12 Psompsonani mwanayo+ kuopera kuti Mulungu angakwiye,Ndipo mungawonongeke ndi kuchotsedwa panjirayo.+Pakuti mkwiyo wake umatha kuyaka mofulumira.+Odala ndi onse amene akuthawira kwa iye.+
2 “Undipsompsone ndi milomo yako,+ chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo kukoma kwake.+