Salimo 92:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+ Yesaya 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Nyumba za njerwa n’zimene zagwazi, koma ife timanga zina za miyala yosema.+ Mitengo ya mkuyu ndi imene yathyoledwayi, koma m’malo mwake ife tipezerapo mitengo ya mkungudza.”+
12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+
10 “Nyumba za njerwa n’zimene zagwazi, koma ife timanga zina za miyala yosema.+ Mitengo ya mkuyu ndi imene yathyoledwayi, koma m’malo mwake ife tipezerapo mitengo ya mkungudza.”+