Nyimbo ya Solomo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mpaka nthawi ya kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka, tembenuka wachikondi wanga. Ukhale ngati mbawala+ kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri amene akutilekanitsa. Nyimbo ya Solomo 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Thamanga wachikondi wanga. Ukhale ngati insa kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri pamene pamamera maluwa onunkhira.”+
17 Mpaka nthawi ya kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka, tembenuka wachikondi wanga. Ukhale ngati mbawala+ kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri amene akutilekanitsa.
14 “Thamanga wachikondi wanga. Ukhale ngati insa kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri pamene pamamera maluwa onunkhira.”+