2 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo. Nyimbo ya Solomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wachikondi wanga akufanana ndi mbawala+ kapena mphoyo yaing’ono. Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma* la nyumba yathu. Akuyang’ana m’mawindo,* akusuzumira pa zotchingira m’mawindo.+ Nyimbo ya Solomo 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Thamanga wachikondi wanga. Ukhale ngati insa kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri pamene pamamera maluwa onunkhira.”+
18 Ndiyeno ana atatu aamuna a Zeruya,+ amene ndi Yowabu,+ Abisai,+ ndi Asaheli+ anali pamenepo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala+ yothamanga m’thengo.
9 Wachikondi wanga akufanana ndi mbawala+ kapena mphoyo yaing’ono. Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma* la nyumba yathu. Akuyang’ana m’mawindo,* akusuzumira pa zotchingira m’mawindo.+
14 “Thamanga wachikondi wanga. Ukhale ngati insa kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri pamene pamamera maluwa onunkhira.”+