Nyimbo ya Solomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe amene mtima wanga umakukonda,+ tandiuza kumene umakadyetsera ziweto,+ kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu ya namalira pakati pa magulu a ziweto za anzako?”
7 “Iwe amene mtima wanga umakukonda,+ tandiuza kumene umakadyetsera ziweto,+ kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu ya namalira pakati pa magulu a ziweto za anzako?”