Nehemiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuwonjezera apo, pa nthawiyo ndinauza anthu kuti: “Mwamuna aliyense pamodzi ndi mtumiki wake azigona mu Yerusalemu,+ ndipo usiku azikhala alonda athu koma masana azigwira ntchito.” Mlaliki 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma+ ngakhale adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona.
22 Kuwonjezera apo, pa nthawiyo ndinauza anthu kuti: “Mwamuna aliyense pamodzi ndi mtumiki wake azigona mu Yerusalemu,+ ndipo usiku azikhala alonda athu koma masana azigwira ntchito.”
12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma+ ngakhale adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona.