Nyimbo ya Solomo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zazikazi zimene zikuchokera kozisambitsa, zonse zitabereka mapasa, popanda imene ana ake afa.+
6 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zazikazi zimene zikuchokera kozisambitsa, zonse zitabereka mapasa, popanda imene ana ake afa.+