Salimo 107:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amadzandira ndipo amayenda peyupeyu ngati munthu woledzera,+Ndipo ngakhale nzeru zawo zonse zimasokonezeka.+ Yesaya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+ Yesaya 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu, dabwani ndipo chitani kukamwa yasa!+ Matani maso anu kuti musaone.+ Iwo aledzera,+ koma osati ndi vinyo. Akudzandira, koma osati chifukwa cha chakumwa choledzeretsa.+
27 Amadzandira ndipo amayenda peyupeyu ngati munthu woledzera,+Ndipo ngakhale nzeru zawo zonse zimasokonezeka.+
14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+
9 Anthu inu, dabwani ndipo chitani kukamwa yasa!+ Matani maso anu kuti musaone.+ Iwo aledzera,+ koma osati ndi vinyo. Akudzandira, koma osati chifukwa cha chakumwa choledzeretsa.+