Salimo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+ Salimo 150:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chopuma chilichonse chitamande Ya.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+ Salimo 150:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chopuma chilichonse chitamande Ya.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+