Yesaya 60:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “M’dziko lako simudzamvekanso zachiwawa. Mkati mwa malire ako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo zipata zako udzazitcha Chitamando. Zekariya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+
18 “M’dziko lako simudzamvekanso zachiwawa. Mkati mwa malire ako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo zipata zako udzazitcha Chitamando.
5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+