2 Mafumu 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Elisa anayamba kupemphera+ kuti: “Inu Yehova, m’tseguleni maso+ chonde kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumiki uja, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo+ oyaka moto. Salimo 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Salimo 125:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wazungulira anthu ake+Ngati mmene mapiri azungulirira Yerusalemu,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+ Yesaya 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+
17 Kenako Elisa anayamba kupemphera+ kuti: “Inu Yehova, m’tseguleni maso+ chonde kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumiki uja, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo+ oyaka moto.
11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
2 Yehova wazungulira anthu ake+Ngati mmene mapiri azungulirira Yerusalemu,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+
26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+