Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 118:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nditsegulireni zipata zachilungamo,+ anthu inu.

      Ndidzalowamo ndipo ndidzatamanda Ya.+

  • Salimo 118:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ichi ndi chipata cha Yehova.+

      Olungama adzalowamo.+

  • Yesaya 60:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Zipata zako zidzakhala zotsegula nthawi zonse.+ Sizidzatsekedwa usana ndi usiku kuti chuma cha mitundu ya anthu chibwere kwa iwe,+ ndipo mafumu awo ndiwo adzakhale patsogolo pochita zimenezi.+

  • Yesaya 62:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tulukani! Tulukani pazipata anthu inu. Lambulani njira yodutsa anthu.+ Konzani msewu. Ukonzeni ndithu. Chotsanimo miyala.+ Akwezereni chizindikiro anthu a mitundu yosiyanasiyana.+

  • Mateyu 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma chipata cholowera ku moyo n’chopapatiza komanso msewu wake ndi wopanikiza, ndipo amene akuupeza ndi owerengeka.+

  • Chivumbulutso 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Odala ndiwo amene achapa mikanjo+ yawo, kuti akhale ndi ufulu wa kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndiponso kuti akalowe mumzindawo kudzera pazipata zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena