Salimo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani,+Pakuti simudzasiya ndithu anthu okufunafunani, inu Yehova.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani,+Pakuti simudzasiya ndithu anthu okufunafunani, inu Yehova.+