Yesaya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzagwetsa mzinda wokhala ndi mipanda yachitetezo italiitali yolimba kwambiri. Adzautsitsa n’kuugwetsera pansi, pafumbi.+ Yeremiya 48:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Anthu inu perekani chizindikiro cha pamsewu kwa anthu a ku Mowabu pakuti adzachoka pamene dziko lawo likusanduka bwinja.+ Mizinda yake idzasanduka chinthu chodabwitsa ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo.+
12 Iye adzagwetsa mzinda wokhala ndi mipanda yachitetezo italiitali yolimba kwambiri. Adzautsitsa n’kuugwetsera pansi, pafumbi.+
9 “Anthu inu perekani chizindikiro cha pamsewu kwa anthu a ku Mowabu pakuti adzachoka pamene dziko lawo likusanduka bwinja.+ Mizinda yake idzasanduka chinthu chodabwitsa ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo.+