Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+ Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+