Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine nditsikira kumeneko+ kudzalankhula nawe.+ Ndidzatengako gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe n’kuuika pa iwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyang’anira anthuwo, kuti usausenze wekhawekha.+

  • 1 Mafumu 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo.

  • Salimo 72:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+

      Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+

  • Yesaya 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena