Salimo 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye akuphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,+Ndipo manja anga akukunga uta wamkuwa.+ Salimo 68:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+Mulungu adalitsike.+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+
35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+Mulungu adalitsike.+