Levitiko 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda mwanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Levitiko 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala+ za m’munda mwanu, ndipo musamatole mphesa zimene zamwazika m’munda mwanu. Zimenezo muzisiyira wovutika ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
9 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda mwanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+
10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala+ za m’munda mwanu, ndipo musamatole mphesa zimene zamwazika m’munda mwanu. Zimenezo muzisiyira wovutika ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”