Yesaya 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khamu la mitundu yonse imene ikuchita nkhondo ndi Ariyeli,+ onse amene akumenyana naye ndi kumumangira nsanja zomenyerapo nkhondo, ndiponso amene akumukhwimitsira zinthu,+ adzaona ngati za m’maloto, za m’masomphenya a usiku.
7 Khamu la mitundu yonse imene ikuchita nkhondo ndi Ariyeli,+ onse amene akumenyana naye ndi kumumangira nsanja zomenyerapo nkhondo, ndiponso amene akumukhwimitsira zinthu,+ adzaona ngati za m’maloto, za m’masomphenya a usiku.