Yesaya 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Taonani! Ambuye woona, Yehova wa makamu, akuthyola nthambi ndipo zikugwa ndi chimkokomo.+ Nthambi zitalizitali zikudulidwa, ndipo zam’mwamba zatsitsidwa.+ Ezekieli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+ Zekariya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lira mofuula, iwe mtengo wofanana ndi mkungudza, chifukwa chakuti mtengo wa mkungudza wagwa, ndiponso mitengo ikuluikulu yawonongedwa.+ Lirani mofuula, inu mitengo ikuluikulu ya ku Basana, chifukwa nkhalango yowirira kwambiri ija yawonongedwa.+
33 Taonani! Ambuye woona, Yehova wa makamu, akuthyola nthambi ndipo zikugwa ndi chimkokomo.+ Nthambi zitalizitali zikudulidwa, ndipo zam’mwamba zatsitsidwa.+
3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+
2 Lira mofuula, iwe mtengo wofanana ndi mkungudza, chifukwa chakuti mtengo wa mkungudza wagwa, ndiponso mitengo ikuluikulu yawonongedwa.+ Lirani mofuula, inu mitengo ikuluikulu ya ku Basana, chifukwa nkhalango yowirira kwambiri ija yawonongedwa.+