Yesaya 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero imvani mawu a Yehova inu anthu odzitama, inu atsogoleri+ a anthu awa amene muli mu Yerusalemu: Yeremiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+
14 Chotero imvani mawu a Yehova inu anthu odzitama, inu atsogoleri+ a anthu awa amene muli mu Yerusalemu:
23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+