Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 18:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iwo anapitiriza kunena kuti: “Bwerani anthu inu, timukonzere chiwembu Yeremiya,+ pakuti chilamulo sichidzachoka pakamwa pa ansembe athu.+ Anthu athu anzeru sadzaleka kupereka malangizo ndiponso aneneri athu sadzaleka kulosera.+ Tabwerani, tiyeni timuukire ndi malilime athu+ ndipo tisamvere mawu ake ngakhale pang’ono.”

  • Mika 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+

  • Luka 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Alembi ndi Afarisi anali kumuyang’anitsitsa+ tsopano, kuti aone ngati angachiritse munthu pa sabata. Iwo anali n’cholinga chakuti am’peze chifukwa.+

  • Luka 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, n’cholinga choti akamukole+ m’mawu ake, kuti akamupereke ku boma ndi kwa bwanamkubwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena