Mateyu 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Afarisi anachoka ndi kukapangana kuti am’kole m’mawu ake.+ Maliko 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake anam’tumizira ena mwa Afarisi ndi a chipani cha Herode,+ kuti akam’kole m’mawu ake.+