Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje. Chivumbulutso 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu, ndi wa Mwanawankhosa.+
6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje.
22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu, ndi wa Mwanawankhosa.+