Mateyu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anthu ochuluka anakhamukira kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, akhungu, osalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana, moti anawakhazika pamapazi ake mochita ngati akum’ponyera, ndipo anawachiritsa onsewo.+
30 Kenako anthu ochuluka anakhamukira kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, akhungu, osalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana, moti anawakhazika pamapazi ake mochita ngati akum’ponyera, ndipo anawachiritsa onsewo.+