Salimo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tcherani khutu lanu kwa ine.+Ndilanditseni mofulumira.+Mukhale thanthwe lolimba kwa ine,+Mukhale nyumba ya mpanda wolimba kuti mundipulumutse.+ Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+
2 Tcherani khutu lanu kwa ine.+Ndilanditseni mofulumira.+Mukhale thanthwe lolimba kwa ine,+Mukhale nyumba ya mpanda wolimba kuti mundipulumutse.+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+