Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje. Luka 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 chifukwa ine ndidzakuuzani mawu oti munene ndi kukupatsani nzeru, zimene otsutsa anu onse sadzatha kuzikana kapena kuzitsutsa.+ Machitidwe 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+
6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje.
15 chifukwa ine ndidzakuuzani mawu oti munene ndi kukupatsani nzeru, zimene otsutsa anu onse sadzatha kuzikana kapena kuzitsutsa.+
13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+