Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “M’tsiku limenelo, pamalo alionse pamene panali mitengo ya mpesa 1,000, yokwana ndalama zasiliva 1,000,+ padzakhala tchire la zitsamba zaminga ndi udzu.+

  • Yeremiya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “‘Pokolola ndidzawafafaniza,’ watero Yehova.+ ‘Mumtengo wa mpesa simudzapezeka mphesa,+ mumtengo wa mkuyu simudzapezeka nkhuyu, ndipo masamba adzafota. Zinthu zimene ndimawapatsa zidzawadutsa.’”

  • Maliro 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo anali kufunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+

      Anali kufunsa chifukwa anali kukomoka m’mabwalo a mzinda ndi kugona pansi ngati anthu ophedwa,

      Ndiponso chifukwa moyo wawo unali kukhuthukira pachifuwa cha amayi awo.

  • Hoseya 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzawononga mitengo yake ya mpesa+ ndi ya mkuyu+ imene iye anali kunena kuti: “Imeneyi ndi mphatso imene amuna ondikonda kwambiri anandipatsa.” Koma ine ndidzachititsa mitengoyo kukhala ngati nkhalango,+ ndipo zilombo zakutchire zidzaidya ndi kuiwononga.

  • Zefaniya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena