Deuteronomo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo ugona pamodzi ndi makolo ako,+ ndipo anthu awa adzaimirira+ ndi kuchita chiwerewere pakati pawo ndi milungu yachilendo ya m’dziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ ndi kuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+ Aheberi 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa chifukwa chimenechi ndinanyansidwa ndi m’badwo umenewo, ndipo ndinati, ‘Nthawi zonse mitima yawo imasochera,+ ndipo sadziwa njira zanga.’+
16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo ugona pamodzi ndi makolo ako,+ ndipo anthu awa adzaimirira+ ndi kuchita chiwerewere pakati pawo ndi milungu yachilendo ya m’dziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ ndi kuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+
10 Pa chifukwa chimenechi ndinanyansidwa ndi m’badwo umenewo, ndipo ndinati, ‘Nthawi zonse mitima yawo imasochera,+ ndipo sadziwa njira zanga.’+