Salimo 78:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+ Machitidwe 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+
55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+
26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+