2 Mafumu 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi ukuganiza kuti ndabwera kudzawononga malo ano popanda chilolezo cha Yehova? Yehova weniweniyo wandiuza+ kuti, ‘Pita ukamenyane ndi dzikolo, ndipo ukaliwononge.’”
25 Kodi ukuganiza kuti ndabwera kudzawononga malo ano popanda chilolezo cha Yehova? Yehova weniweniyo wandiuza+ kuti, ‘Pita ukamenyane ndi dzikolo, ndipo ukaliwononge.’”