2 Mafumu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiika maganizo mwa iye,+ kuti akamva nkhani inayake,+ abwerere kudziko lake. Ndipo mosalephera ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga m’dziko lake.”’”+
7 Ndiika maganizo mwa iye,+ kuti akamva nkhani inayake,+ abwerere kudziko lake. Ndipo mosalephera ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga m’dziko lake.”’”+