Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.

  • 2 Mafumu 19:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kodi sunamve?+ Kuyambira nthawi zakale, izi n’zimene ndidzachite.+

      Ndinakonza zimenezi kuyambira masiku amakedzana.+

      Tsopano ndizichita.+

      Iweyo udzagwira ntchito yosandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, kukhala yopanda anthu ngati milu ya mabwinja.+

  • Yesaya 17:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 M’tsiku limenelo mizinda yake yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri idzakhala ngati malo amene angosiyidwa m’nkhalango. Idzakhala ngati nthambi imene anthu angoisiya chifukwa cha ana a Isiraeli, ndipo idzakhala bwinja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena