Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Atabereka Metusela, Inoki anayendabe ndi Mulungu woona kwa zaka 300. Pa zaka zimenezi, anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.

  • 1 Mafumu 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komanso kuti Yehova adzakwaniritse mawu ake okhudza ine amene analankhula,+ akuti, ‘Ana ako+ akadzasamalira njira zawo, mwa kuyenda+ mokhulupirika*+ pamaso panga ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+

  • 2 Mbiri 31:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena