Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+

  • Levitiko 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+

  • 2 Mafumu 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+

  • 2 Mafumu 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mfumuyo inaimirira pafupi ndi chipilala+ ndipo inachita pangano+ pamaso pa Yehova, kuti adzatsatira+ Yehova ndi kusunga malamulo ake+ ndi maumboni* ake.+ Adzachita zimenezi ndi mtima wonse+ ndi moyo wonse,+ mwa kutsatira mawu a pangano olembedwa m’bukulo.+ Choncho anthu onsewo anavomereza panganolo.+

  • 2 Mbiri 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+

  • Luka 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Onse awiriwo anali olungama+ pamaso pa Mulungu chifukwa choyenda mokhulupirika,+ mogwirizana ndi malamulo onse+ komanso zofunika za m’chilamulo+ cha Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena