2 Mbiri 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anagwira ndi mtima wake wonse+ ntchito iliyonse imene anaiyamba mu utumiki+ wa panyumba ya Mulungu woona ndi m’chilamulo,+ pofunafuna+ Mulungu wake, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.+
21 Anagwira ndi mtima wake wonse+ ntchito iliyonse imene anaiyamba mu utumiki+ wa panyumba ya Mulungu woona ndi m’chilamulo,+ pofunafuna+ Mulungu wake, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.+