2 Mafumu 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti,+ ‘Ndamva pemphero+ limene wapemphera kwa ine lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+ 1 Yohane 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+
20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti,+ ‘Ndamva pemphero+ limene wapemphera kwa ine lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+
14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+